Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Marko 3:1 - Buku Lopatulika

1 Ndipo analowanso m'sunagoge; ndipo munali munthu m'menemo ali ndi dzanja lake lopuwala.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

1 Ndipo analowanso m'sunagoge; ndipo munali munthu m'menemo ali ndi dzanja lake lopuwala.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

1 Yesu adakaloŵanso m'nyumba yamapemphero. M'menemo mudaali munthu wina wopuwala dzanja.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

1 Nthawi inanso analowa mʼsunagoge, ndipo munthu wa dzanja lolumala anali momwemo.

Onani mutuwo Koperani




Marko 3:1
7 Mawu Ofanana  

Ndipo kunachitika, pakumva mfumu mau a munthu wa Mulungu amene anawafuula, kutemberera guwa la nsembe mu Betele, Yerobowamu anatansa dzanja lake ali ku guwalo, nati, Mgwireni iye. Ndipo dzanja lake analitansira kwa iye linauma, kuti sanathe kulifunyatitsanso.


Ndipo iwo analowa mu Kapernao; ndipo pomwepo pa tsiku la Sabata iye analowa m'sunagoge naphunzitsa.


Ndipo analowa m'masunagoge mwao mu Galileya monse, nalalikira, natulutsa ziwanda.


motero Mwana wa Munthu ali mwini tsiku la Sabata lomwe.


M'menemo munagona khamu lalikulu la anthu odwala, akhungu, opunduka miyendo, opuwala.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa