Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Marko 2:6 - Buku Lopatulika

6 Koma anakhalapo ena a alembi akuganizira mumtima mwao,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 Koma anakhalapo ena a alembi akuganizira mumtima mwao,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Koma pamenepo panalinso aphunzitsi ena a Malamulo a Mose. Iwowo adayamba kudzifunsa mumtima mwao kuti,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Ndipo ena mwa aphunzitsi amalamulo anakhala pansi pomwepo, namaganiza mʼmitima mwawo kuti,

Onani mutuwo Koperani




Marko 2:6
6 Mawu Ofanana  

Ndipo Yesu pakuona chikhulupiriro chao ananena ndi wodwala manjenje, Mwana, machimo ako akhululukidwa.


Munthu amene atero bwanji? Achita mwano; akhoza ndani kukhululukira machimo, koma mmodzi, ndiye Mulungu?


Ndipo Yesu pamene anazindikira, ananena nao, Bwanji mutsutsana chifukwa mulibe mkate? Kodi kufikira tsopano simuzindikira, nisimudziwitsa? Kodi muli nayo mitima yanu youma?


ndi kugwetsa matsutsano, ndi chokwezeka chonse chimene chidzikweza pokana chidziwitso cha Mulungu, ndi kugonjetsa ganizo lonse kukumvera kwa Khristu;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa