Marko 2:7 - Buku Lopatulika7 Munthu amene atero bwanji? Achita mwano; akhoza ndani kukhululukira machimo, koma mmodzi, ndiye Mulungu? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Munthu amene atero bwanji? Achita mwano; akhoza ndani kukhululukira machimo, koma mmodzi, ndiye Mulungu? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 “Kodi Iyeyu angalankhule bwanji motere? Si kunyoza Mulungu kumeneku? Ndani angakhululukire machimo, si Mulungu yekha kodi?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 “Nʼchifukwa chiyani munthuyu ayankhula chotere? Iye akuchitira mwano Mulungu! Ndani angakhululukire munthu machimo kupatula Mulungu yekha?” Onani mutuwo |