Marko 2:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo anadza kwa Iye otenga munthu wodwala manjenje, wonyamulidwa ndi anthu anai. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo anadza kwa Iye otenga munthu wodwala manjenje, wonyamulidwa ndi anthu anai. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Anthu ena anai adaanyamula munthu wa ziwalo zakufa, kubwera naye kwa Yesu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Amuna anayi anabwera, atanyamula munthu wofa ziwalo. Onani mutuwo |