Marko 16:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo pamene anakweza maso anaona kuti mwala wakunkhunizidwa, pakuti unali waukulu ndithu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo pamene anakweza maso anaona kuti mwala wakunkhunizidwa, pakuti unali waukulu ndithu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Koma poyang'anitsitsa adaona kuti chimwalacho achigubuduza kale; tsonotu chinali chachikuludi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Koma atakweza maso awo, anaona kuti mwala umene unali waukulu kwambiri wagubuduzidwa kale. Onani mutuwo |