Marko 16:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo analikunena mwa okha, Adzatikunkhunizira ndani mwalawo, pakhomo la manda? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo analikunena mwa okha, Adzatikunkhunizira ndani mwalawo, pakhomo la manda? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Ankafunsana kuti, “Kodi ndani akatichotsere chimwala cha pakhomo pa manda chija?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 ndipo anafunsana wina ndi mnzake kuti, “Kodi akatikugudubuzira mwala pa khomo la manda ndani?” Onani mutuwo |