Marko 16:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo pamene analowa m'manda, anaona mnyamata alikukhala kumbali ya kudzanja lamanja, wovala mwinjiro woyera; ndipo iwo anadabwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo pamene analowa m'manda, anaona mnyamata alikukhala kumbali ya kudzanja lamanja, wovala mwinjiro woyera; ndipo iwo anadabwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Ataloŵa m'mandamo adaona mnyamata wakhala pansi mbali ya ku dzanja lamanja, atavala mkanjo woyera. Azimaiwo adadzidzimuka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Atalowa mʼmanda, anaona mnyamata atavala mwinjiro woyera atakhala ku mbali ya kumanja, ndipo iwo anachita mantha. Onani mutuwo |