Marko 16:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo zitatha izi, anaonekanso Iye m'maonekedwe ena kwa awiri a iwo alikuyenda kupita kumidzi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo zitatha izi, anaonekanso Iye m'maonekedwe ena kwa awiri a iwo alikuyenda kupita kumilaga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Pambuyo pake Yesu, ali ndi maonekedwe osiyana, adaonekera ophunzira ake ena aŵiri, pamene iwowo anali pa ulendo kunja kwa mzinda wa Yerusalemu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Zitatha izi Yesu anaonekera mʼmaonekedwe ena kwa awiri a iwo amene anali ku dera la ku mudzi. Onani mutuwo |