Marko 15:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo khamu la anthu anabwera nayamba kupempha kuti achite monga anali kuwachitira nthawi zonse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo khamu la anthu anabwera nayamba kupempha kuti achite monga anali kuwachitira nthawi zonse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Tsono chikhamu cha anthu chidabwera, nkuyamba kupempha Pilato kuti aŵachitire zomwe adaazoloŵera. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Gulu la anthu linabwera kwa Pilato ndi kumufunsa kuti awachitire zimene amachita nthawi zonse. Onani mutuwo |