Marko 15:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo analipo wina dzina lake Barabasi, womangidwa pamodzi ndi opanduka, amene anapha munthu mumpanduko. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo analipo wina dzina lake Barabasi, wamangidwa pamodzi ndi opanduka, amene anapha munthu mumphandumo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Panali munthu wina, dzina lake Barabasi, amene anali m'ndende pamodzi ndi anthu ena chifukwa choukira Boma ndi kupha anthu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Munthu wotchedwa Baraba anali mʼndende pamodzi ndi anthu owukira amene anapha anthu pa nthawi ya chipolowe. Onani mutuwo |