Marko 15:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo Pilato anawayankha, nanena nao, Kodi mufuna kuti ndikumasulireni mfumu ya Ayuda? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo Pilato anawayankha, nanena nao, Kodi mufuna kuti ndikumasulireni mfumu ya Ayuda? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Pilato adaŵafunsa kuti, “Kodi mukufuna kuti ndikumasulireni Mfumu ya Ayudayi?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 “Kodi mukufuna kuti ndikumasulireni mfumu ya Ayuda?” Pilato anafunsa, Onani mutuwo |