Marko 13:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo Yesu anayamba kunena nao, Yang'anirani kuti munthu asakusocheretseni. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo Yesu anayamba kunena nao, Yang'anirani kuti munthu asakusocheretseni. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Yesu adayamba kuŵauza kuti, “Chenjerani kuti wina aliyense asadzakusokezeni. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Yesu anawawuza kuti, “Chenjerani kuti wina asakunyengeni. Onani mutuwo |