Marko 13:4 - Buku Lopatulika4 Tiuzeni, zinthu izi zidzachitika liti? Ndi chotani chizindikiro chake chakuti zili pafupi pa kumalizidwa zinthu izi zonse? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Tiuzeni, zinthu izi zidzachitika liti? Ndi chotani chizindikiro chake chakuti zili pafupi pa kumalizidwa zinthu izi zonse? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 “Tatiuzani bwino, zimenezi zidzachitika liti? Tidzaonera chiyani kuti zonsezi zili pafupi kuchitika?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 “Tatiwuzani, izi zidzachitika liti? Nanga chizindikiro chakuti zatsala pangʼono kukwaniritsidwa chidzakhala chiyani?” Onani mutuwo |