Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Marko 13:21 - Buku Lopatulika

21 Ndipo pamenepo wina akati kwa inu, Onani Khristu ali pano; kapena, Onani, uko; musavomereze;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

21 Ndipo pamenepo wina akati kwa inu, Onani Khristu ali pano; kapena, Onani, uko; musavomereze;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

21 “Pa nthaŵi imeneyo, wina akadzakuuzani kuti, ‘Ali panotu Khristu uja,’ kapena kuti, ‘Uyo ali apoyo,’ musadzakhulupirire.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

21 Pa nthawi imeneyo, ngati wina adzati kwa inu, ‘Taonani, Khristu ali kuno, kapena, Taonani, uyo ali apoyo!’ musakhulupirire.

Onani mutuwo Koperani




Marko 13:21
8 Mawu Ofanana  

Pakuti ambiri adzafika m'dzina langa, nadzanena, Ine ndine Khristu, nadzasokeretsa anthu ambiri.


Ndipo Ambuye akadapanda kufupikitsa masikuwo, sakadapulumuka munthu mmodzi yense; koma chifukwa cha osankhidwa amene anawasankha, anafupikitsa masikuwo.


pakuti adzauka Akhristu onyenga ndi aneneri onyenga, ndipo adzachita zizindikiro ndi zozizwitsa, kuti akasocheretse, ngati nkutheka, osankhidwa omwe.


Ndipo Iye anati, Yang'anirani musasocheretsedwe; pakuti ambiri adzadza m'dzina langa, nadzanena, Ndine amene; ndipo, Nthawi yayandikira; musawatsate pambuyo pao.


Ndadza Ine m'dzina la Atate wanga, ndipo simundilandira Ine; akadza wina m'dzina lake la iye mwini, iyeyu mudzamlandira.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa