Marko 13:20 - Buku Lopatulika20 Ndipo Ambuye akadapanda kufupikitsa masikuwo, sakadapulumuka munthu mmodzi yense; koma chifukwa cha osankhidwa amene anawasankha, anafupikitsa masikuwo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Ndipo Ambuye akadapanda kufupikitsa masikuwo, sakadapulumuka munthu mmodzi yense; koma chifukwa cha osankhidwa amene anawasankha, anafupikitsa masikuwo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Tsonotu masiku amenewo, Ambuye akadapanda kuŵachepetsa, sakadapulumukapo munthu ndi mmodzi yemwe. Koma masikuwo Mulungu adaŵachepetsa chifukwa cha anthu omwe Iye adaŵasankha. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Ambuye akanapanda kufupikitsa masikuwo, palibe amene akanapulumuka. Koma chifukwa cha osankhidwiratu, amene anawasankha, Iye anawafupikitsa. Onani mutuwo |