Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Marko 13:16 - Buku Lopatulika

16 ndi iye amene ali kumunda asabwere kudzatenga malaya ake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

16 ndi iye amene ali kumunda asabwere kudzatenga malaya ake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

16 Yemwe ali ku munda, asabwererenso ku nyumba kuti akatenge mwinjiro.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

16 Aliyense amene ali ku munda asabwerere kukatenga mkanjo wake.

Onani mutuwo Koperani




Marko 13:16
2 Mawu Ofanana  

ndi iye amene ali pamwamba pa tsindwi asatsike, kapena asalowe kukatulutsa kanthu m'nyumba mwake;


Koma tsoka iwo akukhala ndi pakati, ndi akuyamwitsa ana masiku awo!


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa