Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Marko 13:17 - Buku Lopatulika

17 Koma tsoka iwo akukhala ndi pakati, ndi akuyamwitsa ana masiku awo!

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

17 Koma tsoka iwo akukhala ndi pakati, ndi akuyamwitsa ana masiku awo!

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

17 Ali ndi tsoka akazi amene adzakhale ndi pathupi, ndiponso azimai oyamwitsa ana masiku amenewo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

17 Kudzakhala koopsa mʼmasiku amenewo kwa amayi oyembekezera ndi amayi oyamwitsa!

Onani mutuwo Koperani




Marko 13:17
12 Mawu Ofanana  

Manja a akazi achisoni anaphika ana aoao; anali chakudya chao poonongeka mwana wamkazi wa anthu a mtundu wanga.


Samariya adzasanduka wabwinja, pakuti anapandukana ndi Mulungu wake; iwo adzagwa ndi lupanga, ana ao amakanda adzaphwanyika, ndi akazi ao okhala ndi pakati adzatumbulidwa.


Apatseni, Yehova; mudzapatsa chiyani? Muwapatse mimba yotayataya, ndi mawere ouma.


nanena kwa Iye, Mulinkumva kodi chimene alikunena awa? Ndipo Yesu ananena kwa iwo, Inde: simunawerenge kodi, M'kamwa mwa makanda ndi oyamwa munafotokozera zolemekeza?


ndi iye amene ali kumunda asabwere kudzatenga malaya ake.


Ndipo pempherani kuti kusakhale m'nyengo yachisanu.


Koma tsoka iwo akukhala ndi pakati, ndi iwo akuyamwitsa ana masiku awo! Pakuti padzakhala chisauko chachikulu padziko, ndi mkwiyo pa anthu awa.


Chifukwa taonani masiku alinkudza, pamene adzati, Odala ali ouma ndi mimba yosabala, ndi mawere osayamwitsa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa