Marko 13:15 - Buku Lopatulika15 ndi iye amene ali pamwamba pa tsindwi asatsike, kapena asalowe kukatulutsa kanthu m'nyumba mwake; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 ndi iye amene ali pamwamba pa chindwi asatsike, kapena asalowe kukatulutsa kanthu m'nyumba mwake; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Amene ali padenga pa nyumba yake, asati atsike kuti akatenge chinthu m'nyumba mwakemo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Aliyense amene ali pa denga la nyumba yake asatsike kapena kulowa mʼnyumba kukatenga kanthu kalikonse. Onani mutuwo |