Marko 13:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo mbale adzapereka mbale wake kuti amuphe, ndi atate mwana wake; ndi ana adzayambana ndi akuwabala, nadzawaphetsa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo mbale adzapereka mbale wake kuti amuphe, ndi atate mwana wake; ndi ana adzayambana ndi akuwabala, nadzawaphetsa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Mbale azidzapereka mbale wake kuti aphedwe, bambo azidzapereka mwana wake. Ana azidzaukira makolo ao, mpaka kuŵaphetsa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 “Mʼbale adzapereka mʼbale kuti aphedwe, ndipo abambo adzapereka mwana wawo. Ana adzawukira makolo awo ndi kuwapereka kuti aphedwe. Onani mutuwo |