Marko 13:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo Uthenga Wabwino uyenera uyambe kulalikidwa kwa anthu a mitundu yonse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo Uthenga Wabwino uyenera uyambe kulalikidwa kwa anthu a mitundu yonse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Nkofunika kuti Uthenga Wabwino uyambe walalikidwa kwa anthu a mitundu yonse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Ndipo Uthenga Wabwino uyenera kuyamba walalikidwa kwa anthu a mitundu yonse. Onani mutuwo |