Marko 12:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo anatuma wina; iyeyu anamupha; ndi ena ambiri; ena anawapanda, ndi ena anawapha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo anatuma wina; iyeyu anamupha; ndi ena ambiri; ena anawapanda, ndi ena anawapha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Munthuyo adatumanso wantchito wina, uyu ndiye adangomupheratu. Adachita chimodzimodzi ndi antchito ena ambiri, ena adaŵamenya, ena kuŵapheratu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Anatumizanso wina, ndipo iwo anamupha. Anatumizanso ena ambiri; ena a iwo anawamenya, ena anawapha. Onani mutuwo |