Marko 12:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo anatumanso kapolo wina kwa iwo; ndipo ameneyu anamlasa mutu, namchitira zomchititsa manyazi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo anatumanso kapolo wina kwa iwo; ndipo ameneyu anamlasa mutu, namchitira zomchititsa manyazi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Munthu uja adatumanso wantchito wina, koma alimi aja adamtema m'mutu nkumunyazitsa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Kenaka anatumizanso wantchito wina kwa iwo. Iwo anamumenya munthuyo pamutu ndipo anamuzunza mochititsa manyazi. Onani mutuwo |