Marko 12:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo iwo anamtenga iye, nampanda, namchotsa wopanda kanthu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo iwo anamtenga iye, nampanda, namchotsa wopanda kanthu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Koma alimiwo adamugwira wantchitoyo nammenya, nkumubweza osampatsa kanthu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Koma iwo anamugwira, namumenya ndi kumupirikitsa wopanda kanthu. Onani mutuwo |