Marko 12:21 - Buku Lopatulika21 ndipo wachiwiri anamkwatira, nafa, wosasiya mbeu; ndipo wachitatunso anatero momwemo; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 ndipo wachiwiri anamkwatira, nafa, wosasiya mbeu; ndipo wachitatunso anatero momwemo; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Wachiŵiri adamtenga mai uja, nayenso nkumwalira osasiya mwana. Wachitatunso chimodzimodzi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Wachiwiri anakwatira mkazi wamasiyeyo, koma iye anamwalira wosabereka mwana. Zinali chimodzimodzi ndi wachitatu. Onani mutuwo |