Marko 12:22 - Buku Lopatulika22 ndipo asanu ndi awiriwo analibe kusiya mbeu. Potsiriza pake pa onse mkazinso anafa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 ndipo asanu ndi awiriwo analibe kusiya mbeu. Potsiriza pake pa onse mkazinso anafa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Mpaka asanu ndi aŵiri onse aja adamwalira osasiya mwana. Potsiriza pake mai uja nayenso adamwalira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Kunena zoona, palibe ndi mmodzi yemwe wa asanu ndi awiriwo anasiya ana. Pomaliza, mkaziyo anamwaliranso. Onani mutuwo |