Marko 12:20 - Buku Lopatulika20 Analipo abale asanu ndi awiri; woyamba anakwatira mkazi, nafa, wosasiya mbeu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Analipo abale asanu ndi awiri; woyamba anakwatira mkazi, nafa, wosasiya mbeu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Tsono padaali anthu asanu ndi aŵiri pachibale pao. Woyamba adaakwatira mkazi, namwalira opanda mwana. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Tsopano panali abale asanu ndi awiri. Woyamba anakwatira namwalira wosabereka ana. Onani mutuwo |