Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Marko 12:11 - Buku Lopatulika

11 Ichi chinachokera kwa Ambuye, ndipo chili chozizwitsa m'maso mwathu?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Ichi chinachokera kwa Ambuye, ndipo chili chozizwitsa m'maso mwathu?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Ambuye Mulungu ndiwo adachita zimenezi, ndipo nzotidabwitsa kwambiri.’ ”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Ambuye achita zimenezi, ndipo ndi zodabwitsa mʼmaso mwathu?’ ”

Onani mutuwo Koperani




Marko 12:11
13 Mawu Ofanana  

Ndipo anayankha Labani ndi Betuele, nati, Chatuluka kwa Yehova chinthu ichi; sitingathe kunena ndi iwe choipa kapena chabwino.


Mwala umene omangawo anaukana wakhala mutu wa pangodya.


Ichi chidzera kwa Yehova; nchodabwitsa ichi pamaso pathu.


Penyani mwa amitundu, penyetsetsani, nimudabwe kwakukulu, pakuti ndichita ntchito masiku anu, imene simudzavomera chinkana akufotokozerani.


Pakuti palibe nyanga pakati pa Yakobo, kapena ula mwa Israele; pa nyengo yake adzanena kwa Yakobo ndi Israele, chimene Mulungu achita.


Yesu ananena kwa iwo, Kodi simunawerenge konse m'malembo, Mwala umene anaukana omanga nyumba womwewu unakhala mutu wa pangodya: Ichi chinachokera kwa Ambuye, ndipo chili chozizwitsa m'maso mwathu?


Ndipo anadabwa onse, nathedwa nzeru, nanena wina ndi mnzake, Kodi ichi nchiyani?


kwa iwo amene Mulungu anafuna kuwazindikiritsa ichi chimene chili chuma cha ulemerero wa chinsinsi pakati pa amitundu, ndiye Khristu mwa inu, chiyembekezo cha ulemerero;


Ndipo povomerezeka, chinsinsi cha kuchitira Mulungu ulemu nchachikulu: Iye amene anaonekera m'thupi, anayesedwa wolungama mumzimu, anapenyeka ndi angelo, analalikidwa mwa amitundu, wokhulupiridwa m'dziko lapansi, wolandiridwa mu ulemerero.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa