Marko 11:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo akutsogolera, ndi iwo akutsata, anafuula, Hosana; Wolemekezeka Iye wakudza m'dzina la Ambuye: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo akutsogolera, ndi iwo akutsata, anafuula, Hosana; Wolemekezeka Iye wakudza m'dzina la Ambuye: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Anthu amene adaali patsogolo, ndi amene adaali m'mbuyo, adayamba kufuula kuti, “Ulemu kwa Mulungu. Ngwodala amene alikudza m'dzina la Ambuye. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Amene anatsogola ndi iwo amene ankatsatira ankafuwula kuti, “Hosana! “Odala Iye amene akudza mʼdzina la Ambuye!” Onani mutuwo |