Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Marko 11:8 - Buku Lopatulika

8 Ndimo ambiri anayala zovala zao panjira; ndi ena zitsamba, anazidula m'minda.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Ndimo ambiri anayala zovala zao panjira; ndi ena zitsamba, anazidula m'minda.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Anthu ambiri ankayala zovala zao mu mseu, ena nkumayalika nthambi zamasamba zomwe ankakazithyola ku thengo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Anthu ambiri anayala mikanjo yawo pa msewu, pamene ena anayala nthambi zomwe anadula mʼminda.

Onani mutuwo Koperani




Marko 11:8
5 Mawu Ofanana  

Nafulumira iwo, nagwira yense chofunda chake, nachiyala pokhala iye pachiunda, naomba lipenga, nati, Yehu ndiye mfumu.


Ndipo tsiku loyambali mudzitengere nthambi za mitengo yokoma, nsomo za kanjedza, ndi nthambi za mitengo yovalira, ndi misondodzi ya kumtsinje; ndipo mukondwere pamaso pa Yehova Mulungu wanu masiku asanu ndi awiri.


Ndipo ambirimbiri a mpingowo anayala zovala zao panjira; ndipo ena anadula nthambi za mitengo, naziyala m'njiramo.


Ndipo anabwera naye mwana wa bulu kwa Yesu, naika zovala zao pa iye, ndipo Iye anakhala pamenepo.


Ndipo akutsogolera, ndi iwo akutsata, anafuula, Hosana; Wolemekezeka Iye wakudza m'dzina la Ambuye:


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa