Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Marko 11:7 - Buku Lopatulika

7 Ndipo anabwera naye mwana wa bulu kwa Yesu, naika zovala zao pa iye, ndipo Iye anakhala pamenepo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 Ndipo anabwera naye mwana wa bulu kwa Yesu, naika zovala zao pa iye, ndipo Iye anakhala pamenepo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Ophunzira aja adabwera naye mwanawabuluyo kwa Yesu. Adayala zovala zao pamsana pa bulu uja, Yesu nkukwerapo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 Atafika naye mwana wabulu kwa Yesu, nayika mikanjo yawo pa buluyo, Iye anakwerapo.

Onani mutuwo Koperani




Marko 11:7
8 Mawu Ofanana  

Nafulumira iwo, nagwira yense chofunda chake, nachiyala pokhala iye pachiunda, naomba lipenga, nati, Yehu ndiye mfumu.


Kondwera kwambiri, mwana wamkazi wa Ziyoni; fuula mwana wamkazi wa Yerusalemu; taona, Mfumu yako ikudza kwa iwe; ndiye wolungama, ndi mwini chipulumutso; wofatsa ndi wokwera pabulu, ndi mwana wamphongo wa bulu.


Ndipo anati kwa iwo monga momwe ananena Yesu: ndipo anawalola iwo apite naye.


Ndimo ambiri anayala zovala zao panjira; ndi ena zitsamba, anazidula m'minda.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa