Marko 11:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo anati kwa iwo monga momwe ananena Yesu: ndipo anawalola iwo apite naye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo anati kwa iwo monga momwe ananena Yesu: ndipo anawalola iwo apite naye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Ophunzirawo adaŵayankha monga momwe adaaŵauzira Yesu. Tsono anthuwo adaŵalola kuti ammasule. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Iwo anayankha monga mmene Yesu anawawuzira, ndipo anthu aja anawalola kuti apite. Onani mutuwo |