Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Marko 11:5 - Buku Lopatulika

5 Ndipo ena akuima kumeneko ananena nao, Muchita chiyani ndi kumasula mwana wa bulu?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Ndipo ena akuima kumeneko ananena nao, Muchita chiyani ndi kumasula mwana wa bulu?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Anthu amene adaali pamenepo adaŵafunsa kuti, “Inu nchiyani chimenecho, buluyo mukummasuliranji?”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 anthu ena amene anayima pomwepo anafunsa kuti, “Mukuchita chiyani, kumasula mwana wabuluyo?”

Onani mutuwo Koperani




Marko 11:5
3 Mawu Ofanana  

nanena kwa iwo, Mukani kumudzi wopenyana ndi inu, ndipo pomwepo mudzapeza bulu womangidwa, ndi mwana wake pamodzi naye, masulani iwo, mudze nao kwa Ine.


Ndipo anachoka, napeza mwana wa bulu womangidwa pakhomo, pabwalo m'khwalala, nammasula iye.


Ndipo anati kwa iwo monga momwe ananena Yesu: ndipo anawalola iwo apite naye.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa