Marko 11:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo anachoka, napeza mwana wa bulu womangidwa pakhomo, pabwalo m'khwalala, nammasula iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo anachoka, napeza mwana wa bulu womangidwa pakhomo, pabwalo m'khwalala, nammasula iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Ophunzira aja adapitadi, nakapeza mwanawabuluyo ali chimangirire pa khomo m'mbali mwa mseu, ndipo adayamba kummasula. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Anapita ndipo anakapeza mwana wabulu ali kunja mu msewu waukulu atamumangirira pa chipata. Pamene anamumasula, Onani mutuwo |