Marko 11:10 - Buku Lopatulika10 Wolemekezeka Ufumu ulinkudza, wa atate wathu Davide; Hosana mu Kumwambamwamba. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Wolemekezeka Ufumu ulinkudza, wa atate wathu Davide; Hosana m'Kumwambamwamba. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Udalitsidwe Ufumu wa atate athu Davide umene ulikudza tsopano. Ulemu kwa Mulungu kumwambamwamba.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 “Odala ndi ufumu umene ukubwera wa abambo athu Davide!” “Hosana Mmwambamwamba!” Onani mutuwo |