Marko 11:11 - Buku Lopatulika11 Ndipo Iye analowa mu Yerusalemu, mu Kachisi; ndipo m'mene anaunguza zinthu zonse, popeza ndi madzulo, anatuluka kupita ku Betaniya pamodzi ndi khumi ndi awiriwo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndipo Iye analowa m'Yerusalemu, m'Kachisi; ndipo m'mene anaunguza zinthu zonse, popeza ndi madzulo, anatuluka kupita ku Betaniya pamodzi ndi khumi ndi awiriwo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Yesu ataloŵa m'Yerusalemu, adakaloŵa m'Nyumba ya Mulungu, nayang'anayang'ana zonse. Tsono poti chisisira chinali chitagwa, adatuluka napita ku Betaniya pamodzi ndi ophunzira ake khumi ndi aŵiri aja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Yesu analowa mu Yerusalemu napita ku Nyumba ya Mulungu. Anayangʼana zonse, koma popeza kuti nthawi inali itapita, anatuluka kupita ku Betaniya pamodzi ndi khumi ndi awiriwo. Onani mutuwo |