Marko 11:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo m'mawa mwake, atatuluka ku Betaniya, Iye anamva njala. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo m'mawa mwake, atatuluka ku Betaniya, Iye anamva njala. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 M'maŵa mwake, pamene iwo ankachoka ku Betaniya kuja, Yesu adaamva njala. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Mmawa mwake pamene amachoka ku Betaniya, Yesu anamva njala. Onani mutuwo |