Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Marko 11:21 - Buku Lopatulika

21 Ndipo Petro anakumbukira, nanena naye, Rabi, onani, wafota mkuyuwo munautemberera.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

21 Ndipo Petro anakumbukira, nanena naye, Rabi, onani, wafota mkuyuwo munautemberera.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

21 Apo Petro adakumbuka zijazi, ndipo adauza Yesu kuti, “Aphunzitsi, taonani, mkuyu uja mudautembererawu wauma.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

21 Petro anakumbukira nati kwa Yesu, “Aphunzitsi, taonani! Mtengo wamkuyu munawutemberera uja wafota!”

Onani mutuwo Koperani




Marko 11:21
8 Mawu Ofanana  

Yehova atemberera za m'nyumba ya woipa; koma adalitsa mokhalamo olungama.


Ndipo pakuona mkuyu umodzi panjira, anafika pamenepo, napeza palibe kanthu koma masamba okhaokha; nati Iye kwa uwo, Sudzabalanso chipatso kunthawi zonse. Ndipo pomwepo mkuyuwo unafota.


ndi kulonjeredwa m'misika, ndi kutchedwa ndi anthu, Rabi.


Koma inu musatchedwa Rabi; pakuti Mphunzitsi wanu ali mmodzi, ndipo inu nonse muli abale.


Pomwepo Iye adzanena kwa iwo a kudzanja lamanzere, Chokani kwa Ine otembereredwa inu, kumoto wa nthawi zonse wokolezedwera mdierekezi ndi angelo ake:


Pa mphindikati iyi ophunzira ake anampempha Iye, ndi kunena, Rabi, idyani.


Ngati wina sakonda Ambuye, akhale wotembereredwa. Akudza Ambuye.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa