Marko 10:9 - Buku Lopatulika9 Chifukwa chake chimene Mulungu anachimanga pamodzi, asachilekanitse munthu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Chifukwa chake chimene Mulungu anachimanga pamodzi, asachilekanitse munthu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Tsono zimene Mulungu wazilumikiza pamodzi, munthu asazilekanitse.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Chifukwa chake chimene Mulungu wachilumikiza pamodzi, munthu wina asachilekanitse.” Onani mutuwo |