Marko 10:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo m'nyumba ophunzira anamfunsanso za chinthu ichi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo m'nyumba ophunzira anamfunsanso za chinthu ichi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Pamene adaloŵanso m'nyumba, ophunzira adamufunsanso Yesu za nkhani yomweyi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Pamene analinso mʼnyumba, ophunzira anamufunsa Yesu za izi. Onani mutuwo |