Marko 10:11 - Buku Lopatulika11 Ndipo Iye ananena nao, Munthu aliyense akachotsa mkazi wake, nakakwatira wina, achita chigololo kulakwira mkaziyo; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndipo Iye ananena nao, Munthu aliyense akachotsa mkazi wake, nakakwatira wina, achita chigololo kulakwira mkaziyo; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Iye adaŵauza kuti, “Aliyense amene asudzula mkazi wake nakwatira wina, akuchita chigololo, ndipo akumchimwira mkazi wakeyo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Iye anayankha kuti, “Aliyense amene aleka mkazi wake ndi kukakwatira wina achita chigololo kulakwira mkaziyo. Onani mutuwo |