Marko 10:12 - Buku Lopatulika12 ndipo ngati mkazi akachotsa mwamuna wake, nakwatiwa ndi wina, achita chigololo iyeyu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 ndipo ngati mkazi akachotsa mwamuna wake, nakwatiwa ndi wina, achita chigololo iyeyu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Chimodzimodzinso ngati mkazi asudzula mwamuna wake, kenaka nkukwatiwa ndi wina, nayenso akuchita chigololo.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Ndipo akasiya mwamuna wake ndi kukakwatiwa ndi wina, achita chigololo.” Onani mutuwo |