Marko 10:13 - Buku Lopatulika13 Ndipo analinkudza nato kwa Iye tiana, kuti akatikhudze; ndipo ophunzirawo anawadzudzula. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndipo analinkudza nato kwa Iye tiana, kuti akatikhudze; ndipo ophunzirawo anawadzudzula. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Anthu ena ankabwera ndi ana kwa Yesu kuti aŵakhudze ndi kuŵadalitsa, ophunzira ake nkumaŵazazira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Anthu anabweretsa ana kwa Yesu kuti awadalitse, koma ophunzira anawadzudzula. Onani mutuwo |