Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Marko 10:8 - Buku Lopatulika

8 ndipo awiriwa adzakhala thupi limodzi: kotero kuti salinso awiri, koma thupi limodzi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 ndipo awiriwa adzakhala thupi limodzi: kotero kuti salinso awiri, koma thupi limodzi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 ndipo aŵiriwo adzasanduka thupi limodzi. Choncho tsopano salinso aŵiri, koma thupi limodzi.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 ndipo awiriwo adzakhala thupi limodzi.’ Potero sali awirinso, koma mmodzi.

Onani mutuwo Koperani




Marko 10:8
4 Mawu Ofanana  

Chifukwa chotero mwamuna adzasiya atate wake ndi amake nadzadziphatika kwa mkazi wake: ndipo adzakhala thupi limodzi.


Chifukwa chake chimene Mulungu anachimanga pamodzi, asachilekanitse munthu.


Kapena simudziwa kuti iye wophatikidwa ndi mkazi wachiwerewere ali thupi limodzi? Pakuti awiriwo, ati, adzakhala thupi limodzi.


Koteronso amuna azikonda akazi ao a iwo okha monga ngati matupi a iwo okha. Wokonda mkazi wa iye yekha, adzikonda yekha;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa