Marko 10:7 - Buku Lopatulika7 Chifukwa chake mwamuna adzasiya atate wake ndi amai wake, ndipo adzaphatikizana ndi mkazi wake; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Chifukwa chake mwamuna adzasiya atate wake ndi amai wake, ndipo adzaphatikizana ndi mkazi wake; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Nchifukwa chake mwamuna azisiya atate ndi amai, nakaphatikizana ndi mkazi wake, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 ‘Pa chifukwa ichi mwamuna adzasiya abambo ake ndi amayi ake nakaphatikana ndi mkazi wake, Onani mutuwo |