Marko 10:5 - Buku Lopatulika5 Koma Yesu anati kwa iwo, Chifukwa cha kuuma kwa mitima yanu anakulemberani lamulo ili. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Koma Yesu anati kwa iwo, Chifukwa cha kuuma kwa mitima yanu anakulemberani lamulo ili. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Yesu adati, “Mose adaakulemberani lamulo limeneli chifukwa cha kukanika kwanuku. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Yesu anayankha kuti, “Mose anakulemberani lamulo ili chifukwa chakuwuma kwa mitima yanu. Onani mutuwo |