Marko 1:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo analalikira, kuti, Wondipambana ine mphamvu akudza pambuyo panga, sindiyenera kuwerama kumasula zingwe za nsapato zake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo analalikira, kuti, Wondipambana ine mphamvu akudza pambuyo panga, sindiyenera kuwerama kumasula lamba la nsapato zake ine. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Kulalika kwake ankati, “Pambuyo panga pakubwera wina wamphamvu kuposa ine, mwakuti ineyo ndine wosayenera ngakhale kuŵerama nkumasula zingwe za nsapato zake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Ndipo uthenga wake unali uwu: “Pambuyo panga pakubwera wina wondiposa ine mphamvu. Ine si woyenera kuwerama ndi kumasula zingwe za nsapato zake. Onani mutuwo |