Marko 1:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo Yohane anavala ubweya wa ngamira, ndi lamba lachikopa m'chuuno mwake, nadya dzombe ndi uchi wakuthengo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo Yohane anavala ubweya wa ngamira, ndi lamba lachikopa m'chuuno mwake, nadya dzombe ndi uchi wa kuthengo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Yohaneyo ankavala zovala za ubweya wa ngamira, ndipo ankamangira lamba wachikopa m'chiwuno. Chakudya chake chidaali dzombe ndi uchi wam'thengo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Yohane amavala zovala zopangidwa ndi ubweya wangamira, ndi lamba wachikopa mʼchiwuno mwake, ndipo amadya dzombe ndi uchi wamthengo. Onani mutuwo |