Marko 1:39 - Buku Lopatulika39 Ndipo analowa m'masunagoge mwao mu Galileya monse, nalalikira, natulutsa ziwanda. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201439 Ndipo analowa m'masunagoge mwao m'Galileya monse, nalalikira, natulutsa ziwanda. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa39 Tsono adapita nalalika m'nyumba zamapemphero ku Galileya konseko, ndipo ankatulutsa mizimu yoipa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero39 Potero anayendayenda mu Galileya, kulalikira mʼmasunagoge awo ndi kutulutsa ziwanda. Onani mutuwo |