Marko 1:38 - Buku Lopatulika38 Ndipo ananena nao, Tiyeni kwina, kumidzi ili pafupi apa, kuti ndilalikire komwekonso; pakuti ndadzera ntchito imeneyi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201438 Ndipo ananena nao, Tiyeni kwina, kumidzi ili pafupi apa, kuti ndilalikire komwekonso; pakuti ndadzera ntchito imene. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa38 Koma Iye adaŵauza kuti, “Tiyeni tinke ku midzi ina kufupi konkuno, ndikalalike mau kumenekonso, pakuti ndizo ndidadzera.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero38 Yesu anayakha kuti, “Tiyeni tipite kwina ku midzi ya pafupi kuti ndikalalikirenso kumeneko. Ichi ndi chifukwa chimene ndinabwerera.” Onani mutuwo |