Marko 1:36 - Buku Lopatulika36 Ndipo Simoni ndi anzake anali naye anamtsata, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201436 Ndipo Simoni ndi anzake anali naye anamtsata, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa36 Simoni ndi anzake aja adamlondola komweko. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero36 Simoni ndi anzake anapita kokamufunafuna Iye, Onani mutuwo |